Million-word project: adzayambitsapa 27 April 2024 (Tsiku lowerengapadziko lonse lapansi). Mabukuasanu adzasindikizidwamuchinenero chilichonse kuti apitepatsogolo. HOPE idziperekakukweza bok imodzi mweziuliwonse kwa miyezi 24.Kuwerengera ana akanda, anaokurirako ndi ana ang'onoang'onondikofunikira kwambiri.Zimathandiza ubongo wawo kutiazikula. Makanda amene makoloawo amawawerengera amamvamawu ena miliyoni imodziasanayambe sukulu. Izi zimakulitsamawu awo, zomwezimawathandiza kuphunzirakuwerenga ndi kulemba. Izindizofunikira pophunzira kusikulu.Thandizani mwana wanukukonzekera sukulupomuwerengera tsiku lililonse.
#HOPE-learn
Reading is like giving your child's brain a hug. It helps them grow, learn new things, and it takes their imagination on adventures. Keep turning those pages!
We use cookies to analyze website traffic and optimize your website experience. By accepting our use of cookies, your data will be aggregated with all other user data.